07/06/2026
Zikomo kwambiri Theodorah K. Mtemela ndi team yanu chifukwa chosankha Royal Signature Houses pa wedding preparations yanu.
"Nyumba yabwino si malo ogona okha, koma malo opangira memories yosaiwalika."
Ndife osangalala kukhala gawo la ulendo wanu wapadera.
Congratulations to Frank & Theodora K. Mtemela on your beautiful union. Mulungu adalitse banja lanu. ❤️
Royal Signature Houses – Hospitality with Royal Touch.