Max Complex

Max Complex FOR AFFORDABLE PRICES

Mukufuna chiyani chomwe ku Max Complex kulibe,,Ndalama yanuyo ndi yanu basi,, mukapanda muigwiritsa ntchito mosamala, mu...
14/04/2026

Mukufuna chiyani chomwe ku Max Complex kulibe,,

Ndalama yanuyo ndi yanu basi,, mukapanda muigwiritsa ntchito mosamala, muvutike ndi nokha basi,,

Musazaname kuti simunauzidwe..

Earn once, Spend Once only at MAX COMPLEX ❤️❤️

Tayambo,, Nsinjiro zongophula kumene,,  Max Complex siimaphweketsaZotchipa as always Earn once, Spend Once❤️
14/04/2026

Tayambo,, Nsinjiro zongophula kumene,, Max Complex siimaphweketsa

Zotchipa as always
Earn once, Spend Once❤️

NTHAWI ZINA UMAZAONA NGATI VUTO NDI MADAM KOMA VUTO LIRI LANU KAMBA KOMANGOGULA ZINTHU MALO OSADZIWIKA BWINO..KU Max Com...
25/03/2026

NTHAWI ZINA UMAZAONA NGATI VUTO NDI MADAM KOMA VUTO LIRI LANU KAMBA KOMANGOGULA ZINTHU MALO OSADZIWIKA BWINO..

KU Max Complex NDI MALO OKHAWO AMENE MUNGAGULE KATUNDU WABWINO PA MITENGO YABWINO..

LILOLENI BANJA LANU KUTI LIYAMBE KUDYA MPUNGA POGULA KU MAX COMPLEX,, MUKAGULA KWINAKO,, MUMAONA NGATI MUKUGULA MPUNGA KOMA USALI MPUNGA INU NDIKUMANGODABWA KUTI MPUNGA WANJI OPANDA PFUNGO,, PENA KUMAONA NGATI VUTO NDI AMAYI MAPHIKIDWE..

MUKATERO AMAYI KOMANSO ANA ANU AZAKUDANDAULANI MOYO WAO ONSE..

YAMBANI KUPANGA ZIGANIZO NGATI MUTU WA BANJA POGULA KATUNDU WABWINO KU MAX COMPLEX

TIPEZENI KU AREA 23 ALONG KAMUZU BARRACKS TARMAC ROAD NEAR KACHERE CCAP 🔥🔥🔥💯💪

PENA UMAZAONA NGATI VUTO NDI MADAM KOMA VUTO LIRI LANU KAMBA KOMANGOGULA ZINTHU MALO OSADZIWIKA BWINO..KU Max Complex ND...
25/03/2026

PENA UMAZAONA NGATI VUTO NDI MADAM KOMA VUTO LIRI LANU KAMBA KOMANGOGULA ZINTHU MALO OSADZIWIKA BWINO..

KU Max Complex NDI KU MALO KUMENE MUNGAPEZE KATUNDU WABWINO PA MITENGO YABWINO..

UKAKHALA MPUNGA NDIYE NON CAN BEAT US.

LILOLENI BANJA LANU KUTI LIYAMBE KUDYA MPUNGA POGULA KU MAX COMPLEX..
UDINDO OSAMALIRA BANJA LANU, ULI MMANJA MWANU..
MUSALIDYETSE BANJA LANU ZINTHU ZOONEKA NGATI MPUNGA KOMA USALI MPUNGA,, MKAZI KOMANSO ANA ANU AZAKUDANDAULANI MOYO WAO ONSE..

YAMBANI KUPANGA ZIGANIZO NGATI MUTU WA BANJA..

TIPEZENI KU AREA 23 ALONG KAMUZU BARRACKS TARMAC ROAD NEAR KACHERE CCAP

MAX COMPLEX IS NO JUST A NAME IT'S A BRAND THAT SELLS ORIGINAL COMMODITIES AT A FAIR PRICE ORIGINAL BIC PEN MK700PUROLA ...
25/03/2026

MAX COMPLEX IS NO JUST A NAME

IT'S A BRAND THAT SELLS ORIGINAL COMMODITIES AT A FAIR PRICE

ORIGINAL BIC PEN MK700

PUROLA 2 litre MK15,000

SUPER MAHEU MK2,000

NICE ONE. MK2,000

SOBO 2 litres MK11,000

GLAM & GLORY (SNAIL WHITE LOTION). MK3,500

MOVIT BABY JELLY 200g MK6,500

MPUNGA WA KILOMBERO MK4,000 Per kg

MAZIRA. MK12,000 PER TRAY

TOP SOCIETY BABY JELLY 500g MK12,000

CERELAC Regular MK10,000

BOTSALT 500g MK1,000

SOFTCARE PAMPAZ MK10,000 Pack of 25

And many more including spices like Raja, Garlic powder, Tumeric powder, paprika powder etc

Come and Visit us in Area 23 along the Kamuzu Barracks Tarmac Road near Kachere CCAP or visit Maxcomplex on Google maps

Mpunga timapezeka ndi Kilombero wabwino kwambiri at a Fair Price MK4000 per kg only
13/02/2026

Mpunga timapezeka ndi Kilombero wabwino kwambiri at a Fair Price

MK4000 per kg only

21/01/2026

Affordable prices always

Affordable Prices 🙆Johnson baby jelly MK14,000Top Society baby jelly MK12,000Ingrams MK14, 000Vestline 120grams ,,MK2,50...
03/11/2025

Affordable Prices 🙆

Johnson baby jelly MK14,000
Top Society baby jelly MK12,000
Ingrams MK14, 000
Vestline 120grams ,,MK2,500

25/10/2025
HOPE brings SUCCESS 💪
07/03/2025

HOPE brings SUCCESS 💪

Address

Kamuzu Barracks Tarmac Road
Lilongwe

Opening Hours

Monday 06:00 - 21:00
Tuesday 06:00 - 21:00
Wednesday 06:00 - 21:00
Thursday 06:00 - 21:00
Friday 06:00 - 21:00
Saturday 06:00 - 21:00
Sunday 06:00 - 21:00

Telephone

+265996451145

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Max Complex posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Max Complex:

Share