Lil Praise Mw

Lil Praise Mw Working as "LandMark Real Estate Ltd".

CHIMWAYI CHA NTCHITO!Pakufunika wantchito wa m'nyumba yomwe azikadikira mayi ndi bambo anamwalira ndipo anaikidwa pakhom...
27/07/2026

CHIMWAYI CHA NTCHITO!
Pakufunika wantchito wa m'nyumba yomwe azikadikira mayi ndi bambo anamwalira ndipo anaikidwa pakhomo pompo ana awo amakhala USA komwe amagwira ntchito malipiro azilandila ma dollars tikumane mu comment section mwayi usakusempheni🙌

Dzatsekera tsopano ngalakhe dzakhoza mwachimidzi ndingoti congratulations nde ATI dzutulutsa nyimbo aaaa school iwavuta ...
24/07/2026

Dzatsekera tsopano ngalakhe dzakhoza mwachimidzi ndingoti congratulations nde ATI dzutulutsa nyimbo aaaa school iwavuta bwanji🙌

Bola chisakhale chiwaya cha Nkhuku chifukwa nde mumulakwila mdyombayo🙌😭🤣 Inu mukuganiza chngakhale chiwaya cha Nyama yan...
23/07/2026

Bola chisakhale chiwaya cha Nkhuku chifukwa nde mumulakwila mdyombayo🙌😭🤣 Inu mukuganiza chngakhale chiwaya cha Nyama yanji🙌

Congratulations brother Ngwazi Creations & Shipmark kumwamba kudyeredi Nyama🙏🙏
23/07/2026

Congratulations brother Ngwazi Creations & Shipmark kumwamba kudyeredi Nyama🙏🙏

Mudzutseni Top Fan wa Mess yo angafele k*tulo please 🙏😔
20/07/2026

Mudzutseni Top Fan wa Mess yo angafele k*tulo please 🙏😔

Eeeeshi caption muika nokha inuyo muli mbali iti?🙌
19/07/2026

Eeeeshi caption muika nokha inuyo muli mbali iti?🙌

Happy 86th Birthday his Excellency🎉🥞 🎂More life more blessings Strong Leadership
18/07/2026

Happy 86th Birthday his Excellency🎉🥞 🎂
More life more blessings Strong Leadership

Osamapepesa zinthu zoti m***a kusova ndi mbama aaa nanuso🙌 anyways am a content creator 🙌
17/07/2026

Osamapepesa zinthu zoti m***a kusova ndi mbama aaa nanuso🙌 anyways am a content creator 🙌

Nthawi imeneyo ma graduate Anali okhawo mmudzi mwawo monse anyways mwadziwapo ndani inuyo 🙌
16/07/2026

Nthawi imeneyo ma graduate Anali okhawo mmudzi mwawo monse anyways mwadziwapo ndani inuyo 🙌

Apa mk*ti chimidzi chisanamuthere ndipo asanadziwe k*t ndalama zimakoma bwanji🙌
15/07/2026

Apa mk*ti chimidzi chisanamuthere ndipo asanadziwe k*t ndalama zimakoma bwanji🙌

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lil Praise Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share