Mbayani, Chemussa, Likhubula And Chilimba House For Rent and For Sale

  • Home
  • Malawi
  • Blantyre
  • Mbayani, Chemussa, Likhubula And Chilimba House For Rent and For Sale

Mbayani, Chemussa, Likhubula And Chilimba House For Rent and For Sale Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mbayani, Chemussa, Likhubula And Chilimba House For Rent and For Sale, Real Estate, Likhubula, Blantyre.
(1)

13/01/2023

Ndati ndipepese kwa ma client anthu amene munthawi yomwe munafuna nthandizo lathu ife sitinapezeke
For give us please zinangochitika pazifukwa zina
Kom I promise k*t sizizachitikanso mavuto omwe amapangisawo atha tsopano

Pali njila ina yomwe muthanso kugwilisa tchito potiimbila pa number iyi +265887760884

Manyumba arent akadalipo ambilimbili
Kaya mukufuna kugula Munda, Plot, Malo chabe oti mumangepo nokha Nyumba timapezeka nawonso

Tiyeseni ife ndipo simuzakhumudwa

Manyumba ndi munda wogulisaManyumba wo akupezekera ku msika wanjala, mbayaniPomwe malowo ali ku machinjila
20/10/2022

Manyumba ndi munda wogulisa
Manyumba wo akupezekera ku msika wanjala, mbayani

Pomwe malowo ali ku machinjila

20/10/2022

Cholinga chathu ndik*thandiza inu amene mukufuna funa nyumba za Rent
Tipezeni ife ndip tizakupezerani nyumba yo mosavuta

Ngakhalenso inu amene muli ndi

*Malo
*Ma plot
*Munda
*Estate
Tiuzeni ife ndipo tizakugulisilani mwachangu ndimwadongosolo

Sitikuiwalanso inu amene mukufuna funa
*Malo
*Ma plot
*Munda
*Estate
Tipezeni ndipo simuzakhumudwa

Zonsezi timapanga pamtengo wabwino
Mopandanso chinyengo cholichonse

Address

Likhubula
Blantyre

Telephone

+265887760884

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mbayani, Chemussa, Likhubula And Chilimba House For Rent and For Sale posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category