Mr Reporte at B13 Cumpuss

Mr Reporte at B13 Cumpuss Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mr Reporte at B13 Cumpuss, Real Estate, Namikasi Blantyre, Blantyre.

28/08/2024

Pezani Anu malo abwino komkuja Ku B13 cumpuss okhalako ana a school okha okha bwerana asanathe kuti mudzapeze Anu lero
Namikasi secondary school

01/12/2023

Kwamveka liwu la munthu wa mamuna paselipa Pa 29 November kwamveka kulira kuseliku😭😭

Nyamata wina atageilidwa jist (malo obisika) ixi zachitika kamba ka machezedwe a mkuluyu okonda masewela ogwirana gwirana ask your question

01/12/2023

Nyamata wina

Nyamata wina ku B13 wapezedwa akusamba maliseche (buno buno)(bwamuswe)madzulo atsiku Lina
Nkhaniyi ikuti mkuluyu anali kusamba panja pa mpanda pa tsinde la mtengo izi zaululika pamene atsikana Ena awiri omwe amadekha ku B13 komko atamupeza nyamatayi atazindikira kuti anthu amuona nyamatayi anathawira padzala ndikupitilizabe kusambako izi zayimitsa mutu akatakwe odziwa kuzukuta kamba ka action yomwe nyamatayi anaonetsa eti m'malo mothawira ku bafa lomwe linali pafupi akuthawira padzala oganixa axiti chani Koma Zili chomcho nkhaniyi yatchuka kwambiri maka malo oyandikana nawo 🏞️🏞️ ngati muli ndi funso mungathe kufusa ndipo muzayankhidwa

Mr Reporte at B13 Cumpuss 🎤🎤

Address

Namikasi Blantyre
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mr Reporte at B13 Cumpuss posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category