SupercelI Special Event

SupercelI Special Event Land Selling | Property Management & Development | Land Surveying & Valuation | Architectural Designs

Good morning citizens! Anawo adzuka bwanji lero? Kumawapatsa tchipisi ana kunyumbako kuti asagonekere khosi njonda ina i...
30/12/2023

Good morning citizens!
Anawo adzuka bwanji lero?
Kumawapatsa tchipisi ana kunyumbako kuti asagonekere khosi njonda ina ikawagulira kumsewu.

Kodi kwathu kukatha, dzuwa lathu likazima, ana athuwa adzakhala potani?
Magobo, ma Bank Mkhonde ndi zipeleganyu zija sikufuna koma chifukwa cha mizimu imeneyi.

Gulani malo ku Citizen Real Estate Company kuti ana anu mudzawasiyire mtendere!

Office yathu ndiyotsegula lero!
0994 29 84 40

Winners!!Congratulations to these top 10 engagers this week!Tumizani WhatsApp message ku 0888 41 96 24 kuti mutenge ndal...
29/12/2023

Winners!!
Congratulations to these top 10 engagers this week!

Tumizani WhatsApp message ku 0888 41 96 24 kuti mutenge ndalama zanu za Christmas!

Here are the names!
Gift Piapa, Tinkie Twosixfive, Madalitso Adam, Hæstïñgs Mw, Hastings Born Wa Mangani, Hænzøh-Reælest Rastar Mw, Vill Key, K Iman Amidu, Abdullah Abdul Shakoor, Daphael Wa Bandah

Tabwerani pano 7:30pm muone list ya anthu 10 amene awina Christmas cash pano sabata ino! Osaiwala tiri mkatikati mwa Chr...
29/12/2023

Tabwerani pano 7:30pm muone list ya anthu 10 amene awina Christmas cash pano sabata ino!

Osaiwala tiri mkatikati mwa Christmas Promotion pamene tikumema ma Bank Mkhonde kuti agule plot nkumayilipira pang'ono-pang'ono.

Kudikilira LiVE koma osabwera!Osaonetsa mtima onyanyala ma citizens! Tabwerani pafupi apa mumve amene akulandira mphoto ...
29/12/2023

Kudikilira LiVE koma osabwera!
Osaonetsa mtima onyanyala ma citizens!
Tabwerani pafupi apa mumve amene akulandira mphoto za sabata ino!

BANK MKHONDE IGULE PLOT 2024! Pangani gulu la Bank Mkhonde, SACCO, kapena chipereganyu cha anthu oposera atatu. Dzasankh...
29/12/2023

BANK MKHONDE IGULE PLOT 2024!
Pangani gulu la Bank Mkhonde, SACCO, kapena chipereganyu cha anthu oposera atatu. Dzasankheni ma plot ku Citizen Real Estate Company ku Kanengo, Six Miles, Guzani kapena ku Nathenje monga mwakukonda kwanu molingananso ndi ndalama zimene mumasonkha.

Ma plot mwasankhawo adzaperekedweratu m'mayina amamembala a gululo pamene mukulipira pang'onopang'ono mwezi uliwonse kwa chaka chonse mpaka December 2024.

Kuti mumve zambiri imbani phone kapena WhatsApp 0994 29 84 40

Kapena tipezeni ku office yathu pa Wakawaka ku Lilongwe.

Citizen Real Estate Company,
Building Your Legacy!

Lero 4PM kuli LiVE yogawa mphoto za Christmas komanso kufotokozera za Bank Mkhonde! Mwakonzeka?
29/12/2023

Lero 4PM kuli LiVE yogawa mphoto za Christmas komanso kufotokozera za Bank Mkhonde!
Mwakonzeka?

Good morning on a Friday!Atengeni anzanu, tiyeni ndithu ku lachisanu la mdalitso! Lero tikupanga award madolo oyipatsa f...
29/12/2023

Good morning on a Friday!
Atengeni anzanu, tiyeni ndithu ku lachisanu la mdalitso!

Lero tikupanga award madolo oyipatsa faya pano mphatso za Christmas. Week ikubwerayi tipanganso mphatso za nyuwere.

Kuti mukhale nao mgulu la anthuwa, nkhani yake ndi yomwe ija basi; 'Like, Comment & Share' ma post pamudzi pano!

Service RefinedReal Estate RedefinedCitizen Real Estate Company Building Your Legacy!
28/12/2023

Service Refined
Real Estate Redefined
Citizen Real Estate Company
Building Your Legacy!

Paja madzulo alero tikukambirana zachani top fan?Mkatikati mwa Christmas Promotion!
28/12/2023

Paja madzulo alero tikukambirana zachani top fan?

Mkatikati mwa Christmas Promotion!

Ma Bank Mkhonde ndi zipeleganyu pamene mukuyambiranso mu January muno takufewetserani moyo kuno! Madzulo ano tilengeza z...
28/12/2023

Ma Bank Mkhonde ndi zipeleganyu pamene mukuyambiranso mu January muno takufewetserani moyo kuno!

Madzulo ano tilengeza za momwe mungagulirane ma plot otsika mtengo ndi opereka pang’onopang’ono.

Mulipo angati?
M’masonkha zingati?
Nanga ma plot wo mufuna angati? Olipira kwa nthawi yaitali bwanji?

Tiripano chifukwa cha inu, madzulo ano tikufotokozerani tsatane-tsatane!
0994 29 84 40

Tanena kuti mawa lachisanu tipanga award anthu 10 oyipatsa moto pokonzekera nyuwere, ndi anthu 10 enanso week ikubwerayi...
28/12/2023

Tanena kuti mawa lachisanu tipanga award anthu 10 oyipatsa moto pokonzekera nyuwere, ndi anthu 10 enanso week ikubwerayi.

Zoyenera kuchita ndi zomwe zija monga mwa nthawi zonse; 'Like, Comment & Share' ma post a pa page ino basi.

Nthawi idakalipo, ngati tinafooka tiyeni tidzuke!
Kuli mphoto zambiri kwabasi kuno!

Good morning Akatswiri!Ife tikukumbukira kuti sitinakuoneni inayake pa Christmas monga timayenelera kutero. Koma osadand...
28/12/2023

Good morning Akatswiri!
Ife tikukumbukira kuti sitinakuoneni inayake pa Christmas monga timayenelera kutero. Koma osadandaula, lero ndi lachinayi ndipo mawa ndi lachisanu limene titapange award anthu 10 oyambilira.

Week tikuyamba posachedwayi tipanganso award anthu 10 enanso mpakana mu January!

Zoyenera kuchita ndi zomwe zija basi; ‘Like, Comment & Share,’ ma post athu pa page pano.

Nthawi idakalipo tiye nazoni, mawa pali ndalama, ma T-Shirt ndi zina zambiri zongogawa pano!!

Address

Wakawaka, M1 Road
Lilongwe

Telephone

+265994298440

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when SupercelI Special Event posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to SupercelI Special Event:

Share