11/08/2026
🏡Mukudziwa chani madolo, your security is our priority. Magaye malo awa kulibe zoti akandibela tayamba kumanga🏡
🚨CHIFUKWA CHANI MUPEZEKO YANU PLOT UKU..?🚨
1. Chitetezo chili nyatwa
2. Phindi zochepa mwafika kuchokela pa gateway mall
3. Madzi, magetsi zilipo
4. Msewu waphula mafupi
5. Kwa athu a smart ngati inu(Madolo ngati inu akugula uku)
6. Malo a flat bwino
7. Kapelekedwa kofewa
8. Kuona ndi ulele
✅ NDI Mk 13.5 Million yokha basi mupeza chi 20m by 30m kupeleka pa miyezi inayi
🔥Kodi zabwino ziponse apa magaye🔥
Tiyakhuleni pa
🤙+265991142194 Or +265996537757