13/03/2016
mukudziwitsidwa k*t ngat mwez wamawa tikhala tikuyenda m'midzi kugula masamba achamwamba mtengo ndi k500.00 per kg,koma akgale osamalidwa bwino,oumila pa m'thuzi komaso wa green ngat mulinaye tiuzeni poi number yanu ,zikomo
kudziwitsa anthu za kufunika kwa cham'mwamba ndikomwe angaka gulitse
Kwakwalajacob@gmail. Com
Nkhotakota
JACOB...
Be the first to know and let us send you an email when GREEN POWER FARM Farming And Business posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.